Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZA ZITHUNZI PEJI 28-29: M’bale amene ali m’ndende cifukwa ca cikhulupililo cake akulimbikitsidwa na kalata yocokela kwa a m’banja mwake. Iye ni wokondwa kudziŵa kuti a m’banja mwake sanamuiwale komanso kuti iwo akupitiliza kutumikila Yehova mokhulupilika, ngakhale kuti m’dela lawo muli mavuto a zandale na ciwawa.