Mawu Amunsi
a Kodi kukhala na mtima wamphumphu kumatanthauzanji? N’cifukwa ciani Yehova amaona kuti kukhala na mtima wamphumphu n’kofunika kwambili? Nanga kukhala na mtima wotelo kuli na ubwino wanji kwa ife? Nkhani ino idzafotokoza mayankho a m’Baibo pa mafunso amenewa. Idzafotokozanso zimene zingatithandize kuti tsiku lililonse tizicita zinthu zoonetsa kuti tili na mtima wamphumphu. Ndipo tikatelo, tidzadalitsidwa kwambili.