Mawu Amunsi
a Kodi tingaphunzile ciani kwa Yehova, Yesu, na Msamariya wina wakhate, pankhani yoonetsa kuyamikila? M’nkhani ino, tidzakambilana zitsanzo zimenezi, na zina zambili. Tidzaphunzila cifukwa cake kuonetsa kuyamikila n’kofunika kwambili. Tidzaphunzilanso njila zina zimene tingaonetsele kuyamikila.