Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZEDWA: Kuyamikila munthu kapena cinthu cinacake, kumatanthauza kuzindikila kufunika kwa munthuyo kapena cinthuco. Liwuli limatanthauzanso kuthokoza kocokela pansi pamtima.