Mawu Amunsi
a Ino ni imodzi mwa nkhani zinayi zimene zifotokoze cifukwa cake sitiyenela kukayikila kuti Yehova amatidela nkhawa. Nkhani zitatu zinazo zidzatuluka mu Nsanja ya Mlonda ya May 2019. Mitu ya nkhanizo ni yakuti: “Cikondi na Cilungamo mu Mpingo Wacikhristu,” “Cikondi na Cilungamo M’dziko Loipali” ndi wakuti, “Kulimbikitsa Amene Anacitilidwapo Zolaula.”