Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZEDWA: Malamulo oposa 600 amene Yehova anapatsa Aisiraeli kupitila mwa Mose, amachedwa “Cilamulo,” “Cilamulo ca Mose,” kapena kuti “malamulo.” Kuwonjezela apo, mabuku 5 oyambilila a m’Baibo (Genesis mpaka Deuteronomo), kaŵili-kaŵili amachedwa Cilamulo. Nthawi zina, mawu akuti Cilamulo amagwilitsidwa nchito pochula Malemba onse Aciheberi ouzilidwa.