Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZEDWA: “Kumvelana cisoni” kumatanthauza kuyesetsa kuganizila mmene ena akumvelela na kuyesetsa kumvela monga mmene iwo akumvelela. (Aroma 12:15) M’nkhani ino, mawu akuti “kumvelana cisoni,” ndi akuti “kumvelela ena cifundo” ali na tanthauzo lofanana.