Mawu Amunsi
c Yehova anaonetsanso cifundo kwa atumiki ake ena okhulupilika amene anali opsinjika maganizo komanso amantha. Mwacitsanzo, ganizilani za Hana (1 Sam. 1:10-20) Eliya (1 Maf. 19:1-18), ndi Ebedi-meleki (Yer. 38:7-13; 39:15-18).