Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZEDWA: Liwu lakuti cifundo, limatanthauza kumvelela cisoni munthu amene wakumana na mavuto, kapena amene akuzunzidwa. Cifundo cimasonkhezela munthu kucita zilizonse zimene angathe kuti athandize ena.