Mawu Amunsi
a Cosankha cofunika kwambili cimene mungapange mu umoyo wanu ni ca kubatizika. N’cifukwa ciani kubatizika n’kofunika kwambili? Nkhani ino idzayankha funso limeneli. Idzathandizanso anthu amene akuganizila zobatizika kugonjetsa zopinga zina zimene zingawapangitse kuzengeleza kubatizika.