Mawu Amunsi
a Tinapatsidwa nchito yolalikila uthenga wabwino wa Ufumu na kupanga ophunzila. M’nkhani ino, tidzakambilana mmene tingakwanilitsile mbali zonse za utumiki wathu, ngakhale pamene tikumana na mavuto ambili muumoyo wathu. Tidzakambilananso zimene tingacite kuti tizilalikila mogwila mtima, komanso kuti tizipeza cimwemwe pa nchitoyi.