Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZA ZITHUNZI: Mlongo akucita citsanzo ca ulaliki ca ulendo wobwelelako pa msonkhano wa mkati mwa wiki. Ndiyeno, pamene cheyamani apeleka uphungu, iye akulemba mfundo zofunikila m’kabuku kakuti Kuphunzitsa. Ndipo kumapeto kwa wiki, pamene ali muulaliki, akuseŵenzetsa mfundozo.