Mawu Amunsi
a Tonsefe timakumana na mavuto amene angatilande mtendele wa mumtima. M’nkhani ino, tidzakambilana zinthu zitatu zimene Yesu anacita kuti akhalebe na mtendele wa mumtima. Ifenso ngati ticita zimenezo, tingathe kukhalabe na mtendele wa mumtima, ngakhale kuti timakumana na mavuto aakulu.