Mawu Amunsi
a Mwacikondi, Yehova amatiuza kuti tifunika kupewa mizimu yoipa, cifukwa ingatisoceletse. Kodi mizimu yoipa imawasoceletsa bwanji anthu? Nanga n’zinthu ziti zimene tingacite kuti isatisoceletse? M’nkhani ino, tidzakambilana mmene Yehova amatithandizila kuti tipewe kusoceletsedwa na mizimu yoipa.