Mawu Amunsi
a Munthu amene anacitilidwapo zolaula ali mwana angavutike kwa zaka zambili cifukwa ca zotulukapo zake. M’nkhani ino, tidzakambilana cifukwa cake zili conco. Tidzakambilananso za amene ali pamalo abwino kutonthoza anthu otelo. Potsiliza, tidzakambilana njila zina zabwino zimene tingalimbikitsile anthu amene anacitilidwapo zolaula ali ana.