Mawu Amunsi
a Yehova amatipatsa zinthu zambili zofunika kutamba na kuŵelenga. Nkhani ino idzakuthandizani kudziŵa mmene mungasankhile nkhani zakuti muphunzile. Ndipo muli malangizo othandiza a zimene mungacite kuti muzipindula kwambili na phunzilo lanu laumwini.