Mawu Amunsi
a Nkhani ino na ziŵili zotsatila, zili m’gulu la nkhani zinayi zofotokoza cifukwa cake ndife otsimikiza kuti Yehova ni Mulungu wacikondi komanso wacilungamo. Iye amafuna kuti anthu ake azicitilidwa zinthu mwacilungamo, ndipo amatonthoza anthu amene amacitilidwa zinthu mopanda cilungamo m’dziko loipali.