Mawu Amunsi
e MAWU OFOTOKOZA ZITHUNZI: Yesu ali pa cakudya m’nyumba ya Mfarisi dzina lake Simoni. Mkazi wina, amene mwina ni hule, wanyowetsa mapazi a Yesu na misozi yake, wapukuta mapaziwo na tsitsi lake na kuwapaka mafuta. Simoni akuipidwa na zocita za mkaziyo, koma Yesu akumuikila kumbuyo mkaziyo.