Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, tidzakambilana mmene tingatetezele ana kwa anthu amene amacitila ana zolaula. Tidzaphunzila mmene akulu amatetezela mpingo, na mmene makolo angatetezele ana awo.