Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZEDWA: M’nkhani ino na yotsatila, mawu akuti “wocitilidwa zolaula” atanthauza munthu amene wacitilidwa zolaula ali mwana. Taseŵenzetsa mawu amenewa pofuna kumveketsa bwino mfundo yakuti mwanayo anam’vulaza na kum’pondeleza, komanso kuti iye si wolakwa.