Mawu Amunsi
e Akulu sapempha mwana wocitilidwa zolaula kuti akhalepo pamene akukambilana na munthu amene anam’cita zolaula. Iwo angapemphe kholo lake kapena munthu wina amene mwanayo anamuuza nkhaniyo kuti awafotokozele zimene zinacitika. Mwa ici, amapewa kuwonjezela kuvutika maganizo kwa mwanayo pa zimene zinacitikazo.