Mawu Amunsi
a Nkhani ino idzatithandiza kukhala na cikhulupililo colimba cakuti Yehova yekha ndiye Gwelo la malangizo odalilika. Cinanso, idzatithandiza kuona kuti ngati tiyendela nzelu za dziko, tingakumane na mavuto aakulu, koma ngati titsatila malangizo a m’Baibo, tidzapindula.