Mawu Amunsi
a Maganizo athu nthawi zonse amasonkhezeledwa na cikhalidwe cathu, maphunzilo, na zokumana nazo mu umoyo. Nanga bwanji ngati taona kuti zizolowezi zina zoipa zinazika mizu mwa ife? M’nkhani ino, tidzaphunzila zimene tingacite kuti tithetse zizolowezi zoipa zilizonse zimene tingakhale nazo.