Mawu Amunsi
a Loti, Yobu, ndi Naomi, anakumana na mavuto osiyana-siyana mu umoyo wawo. Koma anatumikila Yehova mokhulupilika. M’nkhani ino, tikambilana zimene tingaphunzilepo pa zimene zinawacitikila. Tikambilananso cifukwa cake tifunika kulankhula molimbikitsa kwa abale na alongo amene akukumana na mavuto, ndiponso kucita nawo zinthu moleza mtima ndi mwacifundo.