Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZA ZITHUNZI: M’bale na mlongo amene angoloŵa kumene m’banja akuceza na m’bale amene anafedwa mkazi camanje-manje. Iwo akukumbukila nthawi pamene anali kusangalala pamodzi na malemuyo.