Mawu Amunsi
b KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Ophunzila a Khristu samangophunzila zimene Yesu anakamba. Koma amayesetsa kucita zimene amaphunzila. Iwo amayesetsa mmene angathele kutsatila mapazi a Yesu, kapena kuti citsanzo cake.—1 Pet. 2:21.