Mawu Amunsi
a Kodi tiyenela kucita ciani ngati boma latiletsa kulambila Yehova? Nkhani ino idzafotokoza zimene tingacite, na zimene tiyenela kupewa n’colinga cakuti tisaleke kulambila Mulungu wathu.