Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Zithunzi zonse zionetsa Mboni zimene zikutumikila m’maiko amene nchito yathu ni yoletsedwa. Pa Cithuzi ici kagulu ka abale na alongo kakucita msonkhano m’cipinda cosungila katundu m’nyumba ya m’bale.