Mawu Amunsi
a Zilibe kanthu kuti tatumikila Yehova kwa zaka zingati, tonse timafuna kupita patsogolo na kukula mwauzimu. Mtumwi Paulo analimbikitsa Akhristu anzake kuti asabwelele m’mbuyo. M’kalata imene iye analembela Afilipi, timapezamo malangizo olimbikitsa amene angatithandize kupilila pa mpikisano wokalandila moyo. M’nkhani ino, tikambilane mmene tingaseŵenzetsele malangizo ouzilidwa amenewo.