Mawu Amunsi
c Popeza mzinda wa Filipi unali pansi pa ulamulilo wa Roma, anthu a mu mzindawo anali na maufulu ena amene nzika za Roma zinali nawo. Conco, fanizo la Paulo linali logwila mtima kwa Akhristu a kumeneko.