Mawu Amunsi
a Kuposa kale lonse, ino ndiyo nthawi yofunika kulimbitsa cikondi pa abale athu. Kalata youzilidwa imene Paulo analembela Afilipi ingatithandize kudziŵa mmene tingakulitsile cikondi pakati pathu, ngakhale m’nthawi zovuta.