Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: M’dziko limene Mboni zilibe ufulu wolalikila poyela, mosamala, m’bale akulalikila uthenga wa Ufumu kwa mnzake. Pamene m’baleyu ali ku nchito, akulalikilanso mnzake wogwila naye nchito pa nthawi yopumula.