Mawu Amunsi
b Mofananamo, abale ambili a maudindo akafika pa msinkhu winawake, amasiyila abale acicepele maudindo awo. Onani nkhani yakuti, “Akhristu Acikulile—Yehova Amayamikila Kukhulupilika Kwanu,” mu Nsanja ya Mlonda ya September 2018, ndiponso yakuti “Khalanibe na Mtendele wa mu Mtima Olo Pamene Zinthu Zasintha,” mu Nsanja ya Mlonda ya October 2018.