Mawu Amunsi
g MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mwa thandizo la Yehova, iwo akuyambanso utumiki wanthawi zonse. Poseŵenzetsa citundu cimene anaphunzila pamene anali amishonale, iwo akulalikila uthenga wabwino kwa anthu ocokela ku dziko lina m’gawo la mpingo wawo.