Mawu Amunsi
a Kudzicepetsa ni limodzi mwa makhalidwe ofunika kwambili amene tifunika kukhala nawo. Kodi kudzicepetsa kumatanthauza ciani? N’cifukwa ciani tiyenela kukhala na khalidwe limeneli? Nanga kusintha kwa zinthu mu umoyo wathu kungayese bwanji kudzicepetsa kwathu? M’nkhani ino, tikambilane mafunso ofunika amenewa.