Mawu Amunsi
a Anthu a Yehova akhala akuyembekezela Aramagedo kwa nthawi yaitali. M’nkhani ino, tikambilane kuti Aramagedo n’ciani. Tikambilanenso zocitika zimene zidzatsogolela ku Aramagedo, ndiponso zimene tingacite kuti tikhalebe okhulupilika pamene mapeto akuyandikila.