Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Pamene zinthu zoopsa zikucitika, (1) sitidzaleka kulalikila malinga ngati zidzakhala zotheka kutelo, (2) tidzapitiliza kucita phunzilo laumwini na kulambila kwa pabanja, komanso (3) tidzapitiliza kudalila citetezo ca Mulungu.