Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, tikambilane zifukwa zimene ziyenela kutisonkhezela kugonjela Yehova. Tikambilanenso mmene akulu, atate, na amayi, angaseŵenzetsele mphamvu ya ulamulilo imene Yehova anawapatsa. Iwo angaphunzile zambili kwa Bwanamkubwa Nehemiya, Mfumu Davide na Mariya, amayi ake a Yesu.