Mawu Amunsi
b KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Anthu amene amacita kukamizidwa kumvela munthu wina, sakondwela na mfundo yakuti tiyenela kugonjela. Koma anthu a Mulungu amaona kuti kugonjela kuli cabe bwino, cifukwa amacita kusankha okha kumvela Yehova.