Mawu Amunsi
f MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Kamnyamata kataila nthawi yaitali kucita maseŵela a pa kompyuta, koma sikanatsilize kugwila nchito zapakhomo na homuweki yake. Amayi ake abwela ku nchito ali olema, ndipo akumulangiza modekha, popanda kukamba mawu aukali.