Mawu Amunsi
a Posacedwa, atsogoleli a maiko adzalengeza kuti akwanitsa kukhazikitsa “bata ndi mtendele” pa dziko. Cilengezo cimeneco cidzakhala cizindikilo cakuti cisautso cacikulu cangotsala pang’ono kuyamba. Koma kodi Yehova afuna kuti tizicita ciani nthawi imeneyo isanafike? Nkhani ino, idzatithandiza kupeza yankho.