Mawu Amunsi
h MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Pa Nkhani Zongocitika Kumene pa TV papelekedwa cilengezo ca “bata ndi mtendele,” ndipo makasitomala mu lesitilanti acita cidwi kwambili na cilengezo cimeneco. M’bale na mkazi wake akupumula mu lesitilantiyo pamene ali mu ulaliki, ndipo sakupusitsidwa na cilengezo cimeneco.