Mawu Amunsi
a Tidziŵa kuti posacedwa, “cisautso cacikulu” cidzayamba. Kodi n’ciani cidzaticitikila pa nthawi imeneyo? Kodi Yehova afuna kuti tizikacita ciani pa nthawiyo? Nanga ni makhalidwe ati amene tifunika kukulitsa pali pano kuti tikakhalebe okhulupilika? Nkhani ino idzayankha mafunso amenewa.