Mawu Amunsi
d Kuti mudziŵe zambili pa zimene zidzacitika nkhondo ya Aramagedo ikadzatsala pang’ono kuyamba, onani nkhani 21 m’buku lakuti Ufumu wa Mulungu Ukulamulila. Ndipo kuti mudziŵe zambili za kuukila kwa Gogi wa Magogi, na mmene Yehova adzatetezela anthu ake pa Aramagedo, onani Nsanja ya Mlonda ya July 15, 2015, mapeji 14-19, komanso mutu 17 na 18 m’buku la Cizungu lakuti Pure Worship of Jehovah—Restored At Last!