Mawu Amunsi
a Ife tonse timakonda kutumikila Yehova. Koma kodi ndife odzipeleka kwa iye yekha? Zosankha zathu n’zimene zimaonetsa ngati ndifedi odzipeleka kwa Yehova yekha. Conco, tiyeni tikambilane zosankha zimene timapanga pa nkhani ya zosangalatsa na ndalama. Kukambilana zimenezi kudzatithandiza kuona ngati ndifedi odzipeleka kwa Yehova yekha.