Mawu Amunsi
a Pamene mapeto akuyandikila, tonse tifunika kulimbitsa ubwenzi wathu na abale na alongo athu. M’nkhani ino, tikambilana zimene tingaphunzilepo pa zimene zinacitikila Yeremiya. Tikambilananso mmene kulimbitsa ubwenzi wathu pali pano kudzatithandizila pa nthawi ya mavuto.