Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: SITEPU 1: M’bale na mlongo afika pa Nyumba ya Ufumu kuti asonkhane pamodzi na Akhristu anzawo. Pa misonkhano imeneyi pamapezeka mzimu wa Yehova. SITEPU 2: Iwo anakonzekela kupelekapo ndemanga pa msonkhanowo. Tifunikanso kutsatila masitepu aŵili amenewa pocita zinthu zina zauzimu zimene takambilana m’nkhani ino, zomwe ni kuŵelenga Mawu a Mulungu, kulalikila, na kupemphela kwa Yehova.