Mawu Amunsi
a Kodi mumadziimba mlandu cifukwa ca zosankha zina zimene munapanga? Kapena mwina nthawi zina zimakuvutani kupanga zosankha na kucita zimene mwasankha? Nkhani ino, idzakuthandizani kugonjetsa zopinga zimenezi na kutsiliza zimene munayamba kucita.