Mawu Amunsi
a Asilikali anali kufunikila cishango kuti akhale otetezeka ku nkhondo. Cikhulupililo cathu cili ngati cishango. Msilikali anali kufunika kusamalila cishango cake. Nafenso tifunika kusamalila cikhulupililo cathu kuti cikhalebe colimba. M’nkhani ino, tidzakambilana zimene tingacite kuti “cishango” cathu “cacikulu cacikhulupililo” cikhalebe colimba.