Mawu Amunsi
a M’buku la Levitiko muli malamulo amene Yehova anapatsa Aisiraeli akale. Popeza ndife Akhristu, sitili pansi pa Cilamulo ca Mose. Ngakhale n’telo, tingapindule na malamulo a m’bukuli. M’nkhani ino, tidzakambilana mfundo zofunika kwambili zimene tingaphunzile m’buku la Levitiko.